LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 September tsa. 6
  • Yesu Analemekeza Atate Wake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yesu Analemekeza Atate Wake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Nyamula Mtengo Wako Wozunzikilapo ndi Kunditsatila Mosalekeza
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Khalani Wodzicepetsa Ena Akakutamandani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Kodi Yesu ni Munthu Wotani?
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • “Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 September tsa. 6
Yesu apeleka ulemelelo kwa Atate wake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOHANE 7-8

Yesu Analemekeza Atate Wake

7:15-18, 28, 29; 8:29

Mu zokamba na zocita zake zonse, Yesu analemekeza Atate wake wakumwamba. Anali kufuna kuti anthu adziŵe kuti uthenga wake unali wocokela kwa Mulungu. Conco, Malemba ndiwo anali maziko a ziphunzitso zake, ndipo kaŵili-kaŵili anali kugwila mau Malemba. Akatamandidwa, Yesu anali kupeleka citamandoco kwa Yehova. Cacikulu kwa iye cinali kukwanilitsa nchito imene Yehova anam’patsa.—Yoh. 17:4.

Tingatengele bwanji citsanzo ca Yesu . . .

  • potsogoza phunzilo la Baibo kapena pophunzitsa pa pulatifomu?

  • pamene anthu ena atitamanda?

  • poganizila mmene tingaseŵenzetsele nthawi yathu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani