LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 2
  • “Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Cikhulupililo Ciyesedwa
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Yehova Anamucha kuti “Bwenzi Langa”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • Mulungu Ayesa Cikhulupililo Ca Abulahamu
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Muzionetsa kuti Mumaona Moyo Mmene Yehova Amauonela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 22-23

“Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”

22:1, 2, 9-12, 15-18

Kuvutika mtima kumene Abulahamu anamvela pokonzekela kupeleka Isaki nsembe, kumatithandiza kudziŵa mmene Yehova anamvelela pamene anapeleka Mwana Wake Yesu Khristu, monga dipo. (Yoh. 3:16) Kodi mawu a Yehova mu vesi 2 aonetsa bwanji cifundo cake?

Zithunzi: 1. Abulahamu wanyamula mpeni, ndipo akuyang’ana kumwamba pamene Isaki ali gone pa guwa. 2. Yesu ali pa mtengo wozunzikikilapo.

Kodi cikondi ca Yehova cimakulimbikitsani kucita ciani?—1 Akor. 6:20; 1 Yoh. 4:11

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani