LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsa. 3
  • Kukwanilitsidwa kwa Maulosi Okhudza Yesu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kukwanilitsidwa kwa Maulosi Okhudza Yesu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Yesu Kristu—Mesiya Wolonjezedwa
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 June tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 15-16

Kukwanilitsidwa kwa Maulosi Okhudza Yesu

Gwilizanitsani cocitika mu umoyo wa Yesu na ulosi umene cocitikaco cinakwanilitsa

COCITIKA

  • Yesu waimilila pamaso pa Pilato

    Maliko 15:3-5

  • Asilikali akucita maele pa zovala za Yesu

    Maliko 15:24

  • Yesu ali pa mtengo, ndipo anthu ambili akumunyoza

    Maliko 15:29, 30

  • Yesu akutsitsidwa kucoka pa mtengo na kukulungiwa nsalu yabwino kwambili

    Maliko 15:43, 46

ULOSI

  • Sal. 22:7

  • Sal. 22:18

  • Yes. 53:7

  • Yes. 53:9

LIMBITSANI CIKHULUPILILO CANU

Ni maulosi ena ati okhudza Yesu amene anakwanilitsidwa? (bhs peji 209; w11 8/15 peji 17

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani