CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 1
Tengelani Kudzicepetsa kwa Mariya
Yehova anapatsa Mariya mwayi wapadela cifukwa anali na mtima wabwino.
Kodi mau amene Mariya anakamba aonetsa bwanji kuti anali . . .
wodzicepetsa?
wa cikhulupililo colimba?
kuwadziŵa bwino Malemba?
munthu woyamikila?