Msonkhano wacigawo wapadela ku Vienna, m’dziko la Austria
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi okwatilana angacite ciani kuti cikwati cawo cikhale colimba?
Lemba: Aef. 5:33
Ulalo: Kodi makolo angalele bwanji ana awo kuti adzakhale anzelu?
○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA
Funso: Kodi makolo angalele bwanji ana awo kuti adzakhale anzelu?
Lemba: Miy. 22:6
Ulalo: Kodi acicepele angapewe bwanji mavuto?
○○● KUBWELELAKO KACIŴILI
Funso: Kodi acicepele angapewe bwanji mavuto?
Lemba: Miy. 4:5, 6
Ulalo: Tingapeze kuti nzelu zotithandiza mu umoyo wathu wa tsiku na tsiku?