CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 11-12
Tengelani Cifundo ca Yesu
N’cifukwa ciani cifundo ca Yesu na kukoma mtima kwake kunali kocititsa cidwi?
Ngakhale kuti Yesu sanakumane na mavuto onse amene anthu ena anapitamo, iye anali kumvetsetsa mmene iwo anali kumvelela
Sanali kucita manyazi kuonetsa poyela mmene anali kumvelela
Sanali kulekelela koma anali kuthandiza