CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AEFESO 1-3
Colinga ca Dongosolo la Mulungu
1:8-10
Dongosolo la Yehova ni makonzedwe amene iye waika kuti agwilizanitse onse a m’banja lake.
Limakonzekeletsa odzozedwa kuti akakhale kumwamba pamodzi na Yesu Khristu, Mutu wawo wauzimu
Limakonzekeletsa amene adzakhala padziko lapansi pamene Ufumu wa Mesiya udzayamba kulamulila
Kodi ningalimbikitse mgwilizano m’gulu la Yehova m’njila ziti?