LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 June tsa. 4
  • Kuyembekezela Moleza Mtima Kumatithandiza Kupilila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kuyembekezela Moleza Mtima Kumatithandiza Kupilila
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Colinga ca Dongosolo la Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Mukhoza Kupilila Pamene Mukuzunzidwa
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Muzikondwela Pogwila Nchito Mwakhama
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 June tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIRO 1-5

Kuyembekezela Moleza Mtima Kumatithandiza Kupilila

N’ciani cinathandiza Yeremiya kupilila ndi kuona zinthu moyenela olo kuti anali kuzunzidwa kwambili?

3:20, 21, 24, 26, 27

  • Anali ndi cidalilo cakuti Yehova ‘adzawelamila’ olapa amene ali pakati pa anthu Ake ndi kuwathandiza pa mavuto awo

  • Anaphunzila ‘kunyamula goli ali mnyamata.’ Munthu akamapilila mayeselo ali wacicepele amakhala wokonzeka kulimbana na zovuta zamtsogolo

Yeremiya apemphela; Anthu a ku Yerusalemu agwidwa ukapolo

Kodi ningakonzekele bwanji zovuta zamtsogolo?

Kodi ningaonetse bwanji kuti nikuyembekezela moleza mtima?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani