M’bale wacinyamata akuphunzitsidwa mu mpingo
Makambilano Acitsanzo
●○○ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu ndiye amacititsa mavuto amene timakumana nawo?
Lemba: Yobu 34:10
Ulalo: N’ndani amacititsa mavuto amene timakumana nawo?
○●○ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: N’ndani amacititsa mavuto amene timakumana nawo?
Lemba: 1 Yoh. 5:19
Ulalo: Kodi Mulungu adzacotsapo bwanji mavuto amene Mdyelekezi anabweletsa?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Kodi Mulungu adzacotsapo bwanji mavuto amene Mdyelekezi anabweletsa?
Lemba: Mat. 6:9, 10
Ulalo: Kodi Ufumu wa Mulungu n’ciani?