LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsa. 7
  • Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • M’kope Ino ya Galamuka!
    Galamuka!—2022
  • Kuyembekezela Moleza Mtima Kumatithandiza Kupilila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Yehova Amakwanilitsa Malonjezo Ake Nthawi Zonse
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 August tsa. 7
Mwamuna na mkazi wake akuyang’ana dzuŵa pamene likuloŵa, ndipo ena akudyela cakudya pamodzi m’Paradaiso

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 4-6

Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu

4:11

Tingaloŵe mu mpumulo wa Yehova mwa kugwila nchito mogwilizana na cifunilo cake cimene cikuvumbulidwa kupitila m’gulu lake. Tifunika kudzifunsa kuti: ‘Kodi nimatani nikalandila uphungu? Kodi nimamvela bwanji ngati kamvedwe ka Malemba kasinthidwa?’

Ni zinthu ziti mu umoyo zimene zimayesa kumvela kwanga?

Abale aŵili akupeleka uphungu wa m’Malemba kwa mlongo; m’bale akucita phunzilo laumwini, ndipo akuganizila masinthidwe amene apangidwa pa kamvedwe kathu ka Malemba
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani