CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 20-22
“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”
21:1-5
Yehova walonjeza kuti adzapanga zinthu zonse kukhala zatsopano.
“Kumwamba kwatsopano”: Boma latsopano limene lidzabweletsa cilungamo na kukonza zinthu zonse pa padziko lapansi
“Dziko lapansi latsopano”: Anthu amene amagonjela ulamulilo wa Mulungu na kutsatila miyezo yake yolungama
“Zinthu zonse . . . n’zatsopano”: Mavuto onse na nkhaŵa zidzalowedwa m’malo na maganizo osangalatsa tsiku lilonse