Abulahamu akuphunzitsa Isaki wacicepele za Yehova
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingadziŵe bwanji za kutsogolo?
Lemba: Yes. 46:10
Ulalo: Ni maulosi ati a m’Baibo amene timaona kuti akukwanilitsika?
○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Ni maulosi ati a m’Baibo amene timaona kuti akukwanilitsika?
Lemba: 2 Tim. 3:1-5
Ulalo: Kodi ni madalitso otani amene anthu adzalandila kutsogolo omwe Mulungu analonjeza?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Kodi ni madalitso otani amene anthu adzalandila kutsogolo omwe Mulungu analonjeza?
Lemba: Yes. 65:21-23
Ulalo: Kodi Mwana wa Mulungu adzacita mbali yanji pobweletsa madalitso amenewa?