Mose na Aroni akamba na Farao
Makambilano Acitsanzo
●○ ULENDO WOYAMBAa
Funso: Kodi tili m’masiku otsiliza?
Lemba: 2 Tim. 3:1-5
Ulalo: N’ciani cidzacitika pambuyo pa masiku otsiliza?
○● ULENDO WOBWELELAKO
Funso: N’ciani cidzacitika pambuyo pa masiku otsiliza?
Lemba: Chiv. 21:3, 4
Ulalo: Tingacite ciani kuti tikalandile madalitso amene Mulungu walonjeza kutsogolo?
a Kuyambila mwezi uno, makambilano acitsanzo azikhala cabe na ulendo woyamba komanso ulendo wobwelelako.