Yosefe adalila Yehova pamene ali m’ndende ku Iguputo
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: N’ciani cimacitika munthu akamwalila?
Lemba: Mlal. 9:5a
Ulalo: Kodi imfa ni mapeto a zonse?
○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Kodi imfa ni mapeto a zonse?
Lemba: Yobu 14:14, 15
Ulalo: Kodi umoyo udzakhala bwanji Mulungu akadzaukitsa okondedwa athu amene anamwalila?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Kodi umoyo udzakhala bwanji Mulungu akadzaukitsa okondedwa athu amene anamwalila?
Lemba: Yes. 32:18
Ulalo: Kodi Mulungu adzabweletsa bwanji mtendele padziko lapansi?