CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 46-47
Thandizo la Cakudya pa Nthawi ya Njala
47:13, 16, 19, 20, 23-25
Masiku ano, anthu m’dzikoli ali na njala yauzimu. (Amosi 8:11) Kupitila mwa Khristu Yesu, Yehova amapeleka cakudya cauzimu ca mwana alilenji.
Mabuku ophunzilila Baibo
Misonkhano ya mpingo
Misonkhano yadela komanso yacigawo
Zomvetsela
Mavidiyo
JW.ORG
JW Broadcasting
Kodi nimadzimana zinthu ziti kuti nizidya cakudya cauzimu pa tebulo la Yehova nthawi zonse?