LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsa. 6
  • Zimene Tingaphunzile pa Zocitika za pa Tsiku la Mwambo Wophimba Macimo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zimene Tingaphunzile pa Zocitika za pa Tsiku la Mwambo Wophimba Macimo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Mfundo Zimene Tingaphunzile mu Buku la Levitiko
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Maguwa Ansembe a pa Cihema Komanso Nchito Yawo pa Kulambila Koona
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 December tsa. 6
Mkulu wa ansembe akuloŵa m’Malo Oyela Koposa atanyamula zofukiza na makala amoto.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 16-17

Zimene Tingaphunzile pa Zocitika za pa Tsiku la Mwambo Wophimba Macimo

16:12-15

Mkulu wa ansembe anali kuseŵenzetsa zofukiza pa Tsiku la Mwambo Wophimba Macimo. Kodi tiphunzilapo ciani pamenepa?

  • Mapemphelo a atumiki okhulupilika a Yehova ali ngati zofukiza. (Sal. 141:2) Mkulu wa ansembe anali kubweletsa zofukiza pamaso pa Yehova mwaulemu kwambili. Mofananamo, nafenso timaonetsa ulemu kwambili popemphela kwa Yehova

  • Mkulu wa ansembe asanapeleke nsembe, coyamba anali kufukiza zofukiza. Mofananamo, Yesu asanapeleke moyo wake monga nsembe, anacita zinazake zimene zinatsegula mwayi wakuti Yehova alandile nsembe yake. Anakhalabe wokhulupilika kwa Yehova pa umoyo wake

Zithunzi: 1. Mwamuna na mkazi wake akupemphela pambuyo pokonzekela ulaliki. 2. Banja limodzi-modzilo likulalikila dilaiva wa taksi posewenzetsa tabuleti.

Kodi ningacite ciani kuti Yehova alandile nsembe yanga?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani