LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 14
  • “Usadzacite Nawo Mgwilizano wa Ukwati”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Usadzacite Nawo Mgwilizano wa Ukwati”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Anaseŵenzetsa Akazi Aŵili Populumutsa Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Citsanzo Cabwino pa Nkhani Yophunzitsa Ena
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Cikondi ca Mulungu Cosasintha Cimatiteteza ku Mabodza a Satana
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso Ndi Moyo?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 14
Mkazi wacikanani akunyengelela mwamuna waciisiraeli kuti agwilizane naye pogwadila fano, ndipo ena amene ali nawo pafupi akucita zinthu zosiyana-siyana zokhudza kulambila mafano.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Usadzacite Nawo Mgwilizano wa Ukwati”

Yehova analamula Aisiraeli kukwatilana kokha na olambila anzawo (Deut. 7:3; w12 7/1 29 ¶2)

Yehova amafuna kuti atumiki ake apewe mavuto na zopweteka (Deut. 7:4; w15 3/15 30-31)

Maganizo a Yehova pankhani ya cikwati sanasinthe (1 Akor. 7:39; 2 Akor. 6:14; w15 8/15 26 ¶12)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi lamulo lakuti tiyenela kukwatila kokha “mwa Ambuye” limanipindulitsa bwanji?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani