LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 13
  • Mmene Cilengedwe Cimaonetsela Cikondi ca Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mmene Cilengedwe Cimaonetsela Cikondi ca Mulungu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Phunzilani Zambili za Yehova Poyang’ana Cilengedwe Cake
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Gwilitsani Nchito Zacilengedwe Pophunzitsa Ana Anu za Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Kodi Mumawaona Makhalidwe Osaoneka a Mulungu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Kodi Mungafotokoze Cikhulupililo Canu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 13
Pamene ali mu ulaliki wa nyumba na nyumba, tate alatila mwana wake mbalame imene yatela mumtengo.

Popeza kuti Yehova waonetsa kuti amatikonda kwambili kupitila m’cilengedwe, tingakhale otsimikiza kuti tikayesetsa kum’tumikila, iye adzatipatsa madalitso oculuka

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Mmene Cilengedwe Cimaonetsela Cikondi ca Mulungu

Tingakhale otangwanika kwambili moti n’kulephela kuganizila zinthu zoculuka zimene Yehova analenga zoonetsa kuti iye ni wacikondi komanso ni wooloŵa manja. Yesu anatilangiza kuti tizicita cidwi na zinthu zacilengedwe, na kuganizilapo mozama zimene tiphunzilapo ponena za Yehova.—Mat. 6:25, 26.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI CILENGEDWE CIMAONETSA CIKONDI CA YEHOVA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

Taphunzila ciani coonetsa kuti Yehova amatikonda tikaona . . .

  • mmene zinthu zacilengedwe zinapangidwila?

  • cifunga dziko?

  • maudzu?

  • mmene nyama zinalengedwela?

  • mphamvu ya kulaŵa, kukhudza, kuona, kumva na kununkhiza?

  • mmene ubongo wathu unapangidwila?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani