LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 16
  • Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • ‘Limba Mtima, Ugwile Nchito Mwamphamvu’
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Nilimbitseni Mtima
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Kulitsani Makhalidwe Aumulungu—Kulimba Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Cilimikani Pamene Mapeto Ayandikila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 16
Mlongo wacitsikana alalikila mnzake wa m’kalasi molimba mtima poseŵenzetsa foni.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta

Kulimba mtima kumatanthauza kuvala zilimbe, kapena kuti kukhala wolimba. Sikutanthauza kuti munthu alibiletu mantha. Koma kumatanthauza kusaopa kucita zinthu ngakhale kuti tili na mantha. Yehova ndiye Gwelo la kulimba mtima kweni-kweni. (Sal. 28:7) Kodi acinyamata angaonetse bwanji kulimba mtima?

ONELELANI VIDIYO YAKUTI TENGELANI CITSANZO CA ANTHU OLIMBA MTIMA, OSATI AMANTHA! PAMBUYO PAKE YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Ni zocitika ziti zofuna kulimba mtima zimene acinyamata amakumana nazo?

  • Ni nkhani ziti za m’Baibo zimene zimatisonkhezela kukhala olimba mtima?

  • Kodi ife na anthu otiona timapindula bwanji ngati ticita zinthu molimba mtima?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani