LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 10
  • “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Inu Akulu—Tengelani Citsanzo ca Gidiyoni
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Gidiyoni Ndi Asilikali Ake 300
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Kudzicepetsa N’kwabwino Kuposa Kunyada
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Makolo Angaphunzile kwa Manowa na Mkazi Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 10
Gidiyoni na amuna amene ali naye akufuula atanyamula miyuni na malipenga.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”

Yehova anapatsa Gidiyoni utumiki wovuta kwambili (Ower. 6:2-6, 14)

Gidiyoni anadziona ngati wosayenelela kucita utumikiwo (Ower. 6:15; w02 2/15 6-7)

Gidiyoni anakwanitsa kucita utumiki umene anapatsidwa cifukwa Yehova anam’patsa mphamvu (Ower. 7:19-22; w05 7/15 16 ¶3)

Abale aŵili amene ali mu ulaliki akufikila mzimayi. M’bale wina ali pa kanjinga ka olemala, ndipo m’bale winayo akumuyendetsa.

Yehova amafuna kuti tiziseŵenzetsa mphamvu zathu pom’lambila. Ngati mphamvu zathu zacepa, mzimu wake woyela umatiwonjezela mphamvu na kutithandiza kupambana.—Yes. 40:30, 31.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani