LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 12
  • Kudzicepetsa N’kwabwino Kuposa Kunyada

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kudzicepetsa N’kwabwino Kuposa Kunyada
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Amaona Atumiki Ake Odzicepetsa Kukhala Amtengo Wapatali
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Kulitsani Makhalidwe Aumulungu—Kudzicepetsa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • “Musamadziganizile Kuposa Mmene Muyenela Kudziganizila”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kudzicepetsa N’kwabwino Kuposa Kunyada

Kudzicepetsa kunathandiza Gidiyoni kulimbikitsa mtendele (Ower. 8:1-3; w00 8/15 25 ¶3)

Gidiyoni anali wodzicepetsa, ndipo anafuna kuti anthu atamande Yehova osati iye (Ower. 8:22, 23; w17.01 20 ¶15)

Kunyada kwa Abimeleki kunapangitsa kuti iye awonongedwe pamodzi na anthu ena (Ower. 9:1, 2, 5, 22-24; w08 2/15 9 ¶9)

Mwininyumba wokwiya akukalipila banja limene likufuna kumulalikila.

Kodi kudzicepetsa kungatithandize bwanji poyankha mwininyumba amene wakwiya?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani