LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 14
  • Kodi Mfumu Yanu N’ndani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mfumu Yanu N’ndani?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Kumvela Kumaposa Nsembe
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kudzikweza Kumanyazitsa Munthu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 14
Mneneli Samueli akulata kumwamba pamene akukamba na Aisiraeli ena.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mfumu Yanu N’ndani?

Modzimva Aisiraeli anapempha kuti akhale na mfumu yaumunthu (1 Sam. 8:4, 5; it-2 163 ¶1)

Aisiraeli sanakhutile kukhala na Yehova monga Wolamulila wawo wosaoneka (1 Sam. 8:7, 8; w11 1/1 27 ¶2)

Yehova anawacenjeza kuti adzakumana na mavuto akadzakhala na mfumu yaumunthu (1 Sam. 8:9, 18; w10 1/15 30 ¶9)

Yehova nthawi zonse wakhala akulamulila monga mfumu yacilengedwe conse. Amalamulila mwacikondi komanso sapeputsa amene amawalamulila. Tikamamvela na kucilikiza ulamulilo wake, tidzalandila madalitso osatha.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi pa umoyo wanga nimaonetsa bwanji kuti nimagonjela ulamulilo wa Yehova?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani