LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 12
  • Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova ni Mulungu Wacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mumapeleka Nsembe Zanu Modzimana?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni

Aminoni anakopeka naye Tamara (2 Sam. 13:1, 2; it-1 32)

Aminoni anagwilila Tamara (2 Sam. 13:10-15; w17.09 5 ¶11)

Abisalomu analamula kuti Aminoni aphedwe (2 Sam. 13:28, 29; it-1 33 ¶1)

Mwamuna na mkazi akucezela pamodzi mosangalala mu lesitilanti.

Kodi anthu amene ali pa cibwenzi angapewe bwanji kudzibweletsela mavuto aakulu? Angatelo mwa kupewa malo komanso mikhalidwe imene ingawapangitse kucita colakwa. Kucita izi kungaonetse kuti ni odziletsa komanso anzelu.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani