LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 14
  • Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kodi Mumapeleka Nsembe Zanu Modzimana?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova ni Mulungu Wacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 14
Abisalomu ali patsogolo pa atumiki ake na Aisiraeli ena, ndipo akukamba na munthu cogwada amene akumuwelamila.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada

Abisalomu anali kufuna kudzipezela ulemelelo (2 Sam. 15:1; it-1 860)

Abisalomu anakopa mitima ya anthu kuti akhale ku mbali yake (2 Sam. 15:2-6; w12 7/15 13 ¶5)

Abisalomu anafuna kulanda atate ake ufumu (2 Sam. 15:10-12; it-1 1083-1084)

Sitiyenela kulola maganizo ofuna zinthu zapamwamba kukula mumtima mwathu. M’malomwake, nthawi zonse tiyenela kupenda zolinga zathu mosamala. M’malo modzifunila ulemelelo, tiyenela kuika zofuna za ena patsogolo.—Afil. 2:3, 4.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani