LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsa. 4
  • Yehova Anapangitsa Zinthu Zosayembekezeleka Kucitika

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Anapangitsa Zinthu Zosayembekezeleka Kucitika
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Mayi Woipa Komanso Wofunitsitsa Ulamulilo Analangidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli na Malile
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Khalanibe Maso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 November tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anapangitsa Zinthu Zosayembekezeleka Kucitika

Pa nthawi ya njala yaikulu, Yehova anakamba kuti tsiku lotsatila padzakhala cakudya coculuka (2 Maf. 7:1; it-1 716-717)

Msilikali wothandiza mfumu ya Isiraeli anasuliza lonjezo la Yehova (2 Maf. 7:2)

Yehova anapangitsa kuti zinthu zosayembekezeleka zicitike (2 Maf. 7:6, 7, 16-18)

Banja la Mboni lili pa malo odyela, ndipo likutamba nyuzi pa TV yokamba za msonkhano wa atsogoleli a maiko. Anthu onse pamalopo akumvetsela nkhaniyo mwachelu.

Yehova amakamba kuti dziko loipali lidzawonongedwa modzidzimutsa komanso mosayembekezeleka. (1 Ates. 5:2, 3) N’cifukwa ciyani kukhulupilila mawu a Yehova n’kofunika?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani