LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 7
  • “Uteteze Mtima Wako”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Uteteze Mtima Wako”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kufuna-funa Nzelu mwa Kuŵelenga Baibo Tsiku Lililonse
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Lembani Mmene Mwapitila Patsogolo
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Zimene Tiphunzilapo pa Mawu Othela Omwe Amuna Okhulupilika Anakamba
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

“Uteteze Mtima Wako”

Mouzilidwa na Mulungu, Solomo analemba kuti : “Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenela kutetezedwa.” (Miy. 4:23) Koma n’zacisoni kuti anthu a Yehova, Aisiraeli, analeka kuyenda pamaso pake “ndi mtima wawo wonse.” (2 Mbiri 6:14) Ngakhale Mfumu Solomo iye mwiniyo analola akazi ake acikunja kupotoza mtima wake moti anayamba kutsatila milungu ina. (1 Maf. 11:4) Kodi tingauteteze bwanji mtima wathu? Uwu ndiwo unali mutu wa nkhani yophunzila mu Nsanja ya Mlonda ya January 2019, tsamba 14-19.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI ZIMENE TINGAPHUNZILE MU NSANJA YA MLONDA—KODI TINGAUTETEZE BWANJI MTIMA WATHU?, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

N’zinthu ziti zimene zikanafooketsa cikhulupililo ca Akhristu a mu vidiyo imeneyi? Nanga nkhani yophunzila imeneyi inawathandiza bwanji kuteteza mitima yawo?

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Zimene Tingaphunzile m’Nsanja ya Mlonda—Kodi Tingauteteze Bwanji Mtima Wathu?” Brent na Lauren akufotokoza zimene zinawacitikila.

    Brent na Lauren

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Zimene Tingaphunzile m’Nsanja ya Mlonda—Kodi Tingauteteze Bwanji Mtima Wathu?” Umjay akuŵelenga zilengezo za nyumba zogulitsa.

    Umjay

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Zimene Tingaphunzile m’Nsanja ya Mlonda—Kodi Tingauteteze Bwanji Mtima Wathu?” Happy akufotokoza zimene zinamucitikila.

    Happy Layou

Kodi nkhani yophunzila imeneyi inakuthandizani bwanji inu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani