LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 7
  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kusonkhana Pamodzi Kumatipindulila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”

Amaziya analemba ganyu asilikali kuti akamuthandize polimbana na adani a Mulungu (2 Mbiri 25:5, 6)

Munthu wa Mulungu anauza Amaziya kuti awabweze asilikaliwo (2 Mbiri 25:7, 8; it-1 1266 ¶6)

Yehova akanamupatsa zambili Amaziya kuposa ndalama zimene anataya (2 Mbiri 25:9, 10)

Zithunzi: Mlongo wacitsikana akuganizila njila ziŵili zosiyana za mmene agwilitsile nchito moyo wake. 1. Akuceza na mnzake amene si Mboni pamene akukaloŵa m’kalasi; akucita ulaliki na mlongo wacikulile. 2. Akuseŵenza mpaka usiku ku nchito yake yolembedwa; akugwila nchito ya mamangidwe ya gulu mosangalala. 3. Akukamba nkhani yofotokozela anthu zinazake kunchito; akutsogoza mzimayi phunzilo la Baibo.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ningadzimane zinthu ziti kuti nicite zambili potumikila Yehova? Nanga ningapeze madalitso otani nikacita zimenezo?’—Mal. 3:10; w21.08 30 ¶16

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani