LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp23 na. 1 tsa. 16
  • Mulungu Walonjeza Kuti Matenda a Maganizo Adzathelatu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mulungu Walonjeza Kuti Matenda a Maganizo Adzathelatu
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Matenda a Maganizo ni Mlili wa Padziko Lonse
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2023
  • Kumwamba Kwatsopano ndi Dziko Lapansi Latsopano Zidzabweletsa Cisangalalo Cacikulu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • ‘Anaona’ Malonjezo a Mulungu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2023
wp23 na. 1 tsa. 16
Wa Mboni za Yehova akuphunzitsa Baibo mzimayi amene ali pacikuto ca magazini ino.

Mulungu Walonjeza Kuti Matenda a Maganizo Adzathelatu

Kupitila m’Baibo, Mulungu amapeleka malangizo na cilimbikitso kwa anthu amene ali na matenda ovutika maganizo.

Koma iye wacita zambili kuposa pamenepa. Walonjeza kuti adzacotselatu zonse zimene zimabweletsa matenda a maganizo.

Mulungu akadzakwanilitsa lonjezo limeneli, sipadzakhalanso kuwawidwa mtima, kupanikizika maganizo, komanso zinthu zoipa zakale “sizidzakumbukilidwanso, ndipo sizidzabwelanso mumtima.”—Yesaya 65:17.

Mboni za Yehova ni zokonzeka kukuthandizani kudziŵa kuti ni liti komanso ni motani mmene Mulungu adzakwanilitsila lonjezo lolimbikitsa limeneli.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani