December Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano December 2019 Makambilano Acitsanzo December 2-8 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 7-9 Khamu Lalikulu Losaŵelengeka Likudalitsidwa na Yehova December 9-15 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 10-12 ‘Mboni Ziŵili’ Zinaphedwa, Kenako Zinakhalanso na Moyo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Dzikolo ‘Linameza Mtsinje’ December 16-22 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 13-16 Musamaope Zilombo Zoopsa December 23-29 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 17-19 Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse December 30, 2019–January 5, 2020 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 20-22 “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Khalani Okonzeka Kusintha Ulaliki