August Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, ka August 2020 Makambilano Acitsanzo August 3-9 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 13-14 “Cilimikani ndi Kuona Cipulumutso ca Yehova” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Cilimikani Pamene Mapeto Ayandikila August 10-16 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 15-16 Tamandani Yehova mwa Kuimba Nyimbo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Tamandani Yehova Monga Mpainiya August 17-23 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 17–18 Amuna Odzicepetsa Amaphunzitsa Ena Nchito na Kuwagaŵila Maudindo August 24-30 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 19–20 Mfundo za Malamulo Khumi Zotithandiza August 31–September 6 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 21-22 Muzionetsa kuti Mumaona Moyo Mmene Yehova Amauonela