Mose watambasula dzanja lake kuti agawanitse Nyanja Yofiila
Makambilano Acitsanzo
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti citonthozo tikafeledwa?
Lemba: 2 Akor. 1:3, 4
Ulalo: N’ciani cimacitika munthu akamwalila?
○● ULENDO WOBWELELAKO
Funso: N’ciani cimacitika munthu akamwalila?
Lemba: Mlal. 9:5, 10
Ulalo: Kodi tili na ciyembekezo canji cokhudza akufa?