September Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, ka September 2020 Makambilano Acitsanzo September 7-13 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 23-24 Usatsatile Khamu la Anthu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Pewani Kufalitsa Nkhani za Bodza September 14-20 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EKSODO 25-26 Cimene Cinali Cofunika Kwambili m’Cihema September 21-27 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 27–28 Kodi Tingaphunzile Ciani pa Zovala za Ansembe? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Anthu Amene Safuna Kutuluka m’Nyumba September 28–October 4 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EKSODO 29–30 Kupeleka kwa Yehova Copeleka UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kodi Mungapeleke Nthawi na Mphamvu Zanu?