LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 116
  • Kuwala Kukuwonjezereka

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kuwala Kukuwonjezereka
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Kuwala Kuwonjezeleka
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • “Onetsani Kuwala Kwanu”
    Imbirani Yehova
  • Khulupilila Coonadi Iwe Mwini
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi
    Imbirani Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 116

Nyimbo 116

Kuwala Kukuwonjezereka

(Miyambo 4:18)

1. Aneneri akale ankafuna

Kudziwa za Yesu Mesiya.

Mzimu wa M’lungu unaneneratu

Kuti adzatipulumutsa.

Nthawi yafika, akulamulira.

Umboni wake ulipo.

Kudziwa zimenezi ndi mwayi

Waukulu womwe tili nawo.

(KOLASI)

Kuwala kwa panjira yathu

Kukuwonjezerekadi.

Zomwe M’lungu akuulula

Zimatitsogoleradi.

2. Ambuye wathu wasankha kapolo.

Ndi mmene amatidyetsera.

Ndipo m’kupita kwa nthawi kuwala

Kwa cho’nadi kwawonjezeka.

Pano tikuyenda molimba mtima,

Mowala ngati masana.

Tikuthokoza Yehova chifukwa

Cho’nadi chake watipatsa.

(KOLASI)

Kuwala kwa panjira yathu

Kukuwonjezerekadi.

Zomwe M’lungu akuulula

Zimatitsogoleradi.

(Onaninso Aroma 8:22; 1 Akor. 2:10; 1 Pet. 1:12.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani