LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 53
  • Tigwire Ntchito Mogwirizana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tigwire Ntchito Mogwirizana
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tisunge Umodzi Wathu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mtendere Wathu Wamtengo Wapatali
    Imbirani Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 53

Nyimbo 53

Tigwire Ntchito Mogwirizana

(Aefeso 4:3)

1. Tili m’gulu la Yehova,

Ndifedi osangalala,

Komanso ogwirizana,

N’zosangalatsadi.

Timasangalala

Ndi mgwirizano.

Zoti tichite n’zambiri,

Yesu atitsogolera.

Titumikire momvera,

Mogwirizananso.

2. Popempherera umodzi,

N’kukhala okoma mtima,

Chikondi chathu chikula,

Tidzasangalala.

Mtendere n’ngwabwino,

Utsitsimula.

Inde tikamakondana,

Tidzapezadi mtendere.

Tikhala ogwirizana,

Pomutumikira.

(Onaninso Mika 2:12; Zef. 3:9; 1 Akor. 1:10.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani