LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 109
  • Tizikondana ndi Mtima Wonse

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tizikondana ndi Mtima Wonse
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Tingalimbikitsile Cikondi Cathu pa Ena
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • “Uzikonda Yehova Mulungu Wako”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Musalole Kuti Cikondi Canu Cizilale
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Tizikondana Kwambiri Kuchokera Mumtima
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 109

NYIMBO 109

Tizikondana ndi Mtima Wonse

Yopulinta

(1 Petulo 1:22)

  1. 1. Tikakhala na cikondi

    Tikondweletsa Yehova,

    Cifukwa iye n’cikondi—

    Amatikondadi.

    Ngati timakonda ena

    Sitidzacita kaduka.

    Koma ise tidzakhala

    Mabwenzi abwino.

    Ena akavutika,

    Tisacedwe kuŵathandiza.

    Ngati ena afo’ka

    Timamvela cifundo.

    Monga Atate Yehova,

    Timaonetsa cikondi.

    Tikonde abale athu

    Na cikondi coona,

    Na mtima wathu wonse.

(Onaninso 1 Pet. 2:17; 3:8; 4:8; 1 Yoh. 3:11.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani