LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsa. 5
  • Yehova Sadzanyoza Munthu Wosweka Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Sadzanyoza Munthu Wosweka Mtima
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Chimo ya Mfumu Davide
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Yehova Amathandiza Odwala
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Mavuto M’nyumba Ya Davide
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 June tsa. 5

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 45-51

Yehova Sadzanyoza Munthu Wosweka Mtima

Cikumbumtima cinamuvutitsa kwambili Davide atamvela fanizo la munthu wolemela amene anatenga kamwana ka nkhosa ka munthu wosauka

Salimo 51 inalembedwa ndi Davide pambuyo pakuti mneneli Natani wamuuza za chimo lalikulu limene anacita ndi Batiseba. Cikumbumtima cinamuvutitsa kwambili Davide, cakuti anavomeleza chimo lakelo modzicepetsa. —2 Sam. 12:1-14.

Davide anacimwa, koma zinali zotheka kulandila thandizo lauzimu

51:3, 4, 8-12, 17

  • Asanalape ndi kuvomeleza chimo, cikumbumtima cinali kumuvutitsa kwambili

  • Anavutika kwambili cifukwa cosayanjidwa ndi Mulungu, cakuti anali kudziona ngati munthu amene waphwanyidwa mafupa

  • Anafunitsitsa kukhululukidwa, kulandila thandizo lauzimu, ndi kukhala ndi cimwemwe cimene anali naco poyamba

  • Anapempha Yehova modzicepetsa kuti amuthandize kukhala ndi mtima womvela

  • Anali ndi cidalilo cakuti Yehova adzamukhululukila

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani