LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 3
  • Tamandani Yehova Womvela Pemphelo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tamandani Yehova Womvela Pemphelo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • 61:1, 8
  • Yandikilani kwa Mulungu Kupitila M’pemphelo
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • Pitilizani Kupemphela Kuti Mulungu Akuyanjeni
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 60–68

Tamandani Yehova Womvela Pemphelo

Zimene timalonjeza Yehova, tizizichula m’mapemphelo athu

61:1, 8

  • Kuchula malonjezo athu m’pemphelo kudzatithandiza kuwasunga

  • Kudzipeleka kwa Mulungu ndilo lonjezo lofunika kwambili kuposa onse

Hana apemphela

Hana

Onetsani kuti mumam’dalila Yehova mwa kumukhutulila nkhawa zanu zonse popemphela

62:8

  • Pemphelo locokela pansi pa mtima n’limene timafotokoza mmene timvelela

  • Kufotokoza zinthu mosapita mbali m’pemphelo, kudzatithandiza kudziŵa kuti Yehova wayankha pemphelo lathu

Yesu apemphela

Yesu

Yehova amamvela mapemphelo a anthu a maganizo oyenela

65:1, 2

  • Yehova amamvela mapemphelo a “anthu osiyanasiyana”, amene amafuna kumudziŵa ndi kucita cifunilo cake

  • Tingapemphele kwa Yehova nthawi iliyonse imene tifuna

Koneliyo apemphela

Koneliyo

Lembani nkhani zimene mufuna kuchula m’mapemphelo anu:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani