Paulo na Baranaba aimilila pamaso pa Serigio Paulo
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 12-14
Paulo na Baranaba Apanga Ophunzila Kumadela Akutali
13:12, 48; 14:1, 21, 22
Ngakhale kuti Paulo na Baranaba anatsutsidwa mwamphamvu, anacita khama kuthandiza anthu ofatsa kukhala Akhristu
Iwo analalikila anthu a zikhalidwe zosiyana-siyana
Analimbikitsa ophunzila atsopano kuti “akhalebe m’cikhulupililo”