LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 January tsa. 8
  • Yehova Anatiphunzitsa Kulela Bwino Ana Athu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Anatiphunzitsa Kulela Bwino Ana Athu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Makolo—Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Kodi Muyenela Kucita Ciyani Kuti Banja Lanu Likhale Lacimwemwe?—Mbali 2
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Inu Makolo—Thandizani Ana Anu Kukonda Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Makolo, Phunzitsani Ana Anu Zimene Afunika Kudziŵa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 January tsa. 8
Abilio na Ulla Amorim

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Yehova Anatiphunzitsa Kulela Bwino Ana Athu

Kodi makolo angaphunzile ciani kwa Atate wawo wakumwamba Yehova, cimene cingawathandize kulela bwino ana awo? Tambitsani vidiyo yakuti Yehova Anatiphunzitsa Kulela Bwino Ana Athu, kenako yankhani mafunso otsatilawa okhudza m’bale Abilio na mlongo Ulla Amorim:

Abilio na Ulla Amorim pa tsiku lawo la cikwati, ali na ana awo, ndipo m’modzi wa ana awo ali na mkazi wake mu ulaliki
  • Kodi zimene iwo anapitamo ali ana, zinawathandiza bwanji kukhala makolo abwino?

  • Ni zosangalatsa zabwanji za pa ubwana zimene ana awo amakumbukila?

  • Kodi m’bale Abilio na mlongo Ulla analiseŵenzetsa bwanji lemba la Deuteronomo 6:6, 7?

  • N’cifukwa ciani sanali kungowauza zocita ana awo?

  • Kodi anawathandiza bwanji ana awo kupanga tsogolo labwino?

  • Iwo nthawi zonse anali kulimbikitsa ana awo kucita utumiki wanthawi zonse. Kodi izi zinatanthauza kudzimana ciani monga makolo? (bt peji 178 pala. 19)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani