LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsa. 2
  • Kodi Kuonetsa Cikondi Cacikhristu Kumatanthauza Ciani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Kuonetsa Cikondi Cacikhristu Kumatanthauza Ciani?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Chikondi cha Mulungu N’chosatha
    Imbirani Yehova
  • Cikondi Cokhulupilika ca Mulungu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 March tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 12-14

Kodi Kuonetsa Cikondi Cacikhristu Kumatanthauza Ciani?

12:10, 17-21

Wina akatilakwila, cikondi cacikhristu cimatithandiza kuti tisabwezele, komanso kuti timucitilebe zinthu mokoma mtima. Paja Baibo imati: “Ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse cakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse cakumwa. Pakuti mwa kutelo udzamuunjikila makala a moto pamutu pake.” (Aroma 12:20) Kukoma mtima kumene tingaonetse kwa munthu amene watilakwila, kungam’pangitse kumva kuipa pa zimene waticitila.

Mlongo akunyozedwa na mzake wa kunchito, m’madzulo tsikulo iye akukamba na mkulu, ndipo tsiku lotsatila mlongoyo akukamba mokoma mtima kwa mnzake wa kunchito

Kodi munamvela bwanji pamene munakhumudwitsa munthu wina mosadziŵa, koma iye anayankhabe mokoma mtima?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani