CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 PETULO 1-2
“Mukhale Oyela”
1:14-16
Tiyenela kukhala oyela, kapena kuti aukhondo, kuti kulambila kwathu kukhale kovomelezeka kwa Yehova. Kodi kumatanthauzanji kukhala woyela . . .
mwauzimu?
m’makhalidwe?
mwakuthupi?