October 14-20
1 PETULO 1-2
Nyimbo 29 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mukhale Oyela”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Petulo.]
1 Pet. 1:14, 15—Zokhumba zathu na khalidwe lathu zifunika kukhala zoyela (w17.02 9 ¶5)
1 Pet. 1:16—Timayesetsa kutengela citsanzo ca Mulungu wathu woyela (lvs 77 ¶6)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
1 Pet. 1:10-12—Kodi tingaonetse bwanji khama monga la aneneli na angelo? (w08 11/15 21 ¶10)
1 Pet. 2:25—Kodi Woyang’anila Wamkulu Koposa n’ndani? (it-2 565 ¶3)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Pet. 1:1-16 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Khala Bwenzi la Yehova—Khala Woyela ndi Waudongo: (6 min.) Tambitsani vidiyoyi. Kenako, itanilani ku pulatifomu ana amene munawakonzekeletsa, na kuwafunsa mafunso aya: Kodi Yehova anakonza bwanji malo a zinthu zonse? N’ciani cimathandiza mvuu kukhala zaukhondo? N’cifukwa ciani ufunika kuyeletsa cipinda cako?
“Yehova Amakonda Anthu Aukhondo”: (9 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Mulungu Amakonda Anthu Oyela.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 87
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 39 na Pemphelo