LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • Ndandanda ya Mlungu wa September 28
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015 | September
    • Ndandanda ya Mlungu wa September 28

      MLUNGU WA SEPTEMBER 28

      Nyimbo 73 ndi Pemphelo

      Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

      cl mutu 16 ndime 1-9 (Mph. 30)

      Sukulu ya Ulaliki:

      Kuŵelenga Baibulo: 2 Mafumu 23-25 (Mph. 8)

      Na. 1: 2 Mafumu 23:8-15 (Mph. 3 kapena zocepelapo)

      Na. 2: Kodi Angelo Amagwila Nchito Yanji Pokwanilitsa Cifunilo ca Mulungu? (Mph. 5)

      Na. 3: Muzitumikila Yehova Mokhulupilika—(w11 7/15 tsa. 31 ndime 16) (Mph. 5)

      Msonkhano wa Nchito:

      Lemba la Mwezi: “Kucitila umboni mokwanila za uthenga wabwino.”—Machitidwe 20:24.

      Nyimbo 93

      Mph. 10: Paulo ndi Atumiki Anzake Anacitila Umboni Mokwanila ku Filipi. Kukambilana. Ŵelengani Machitidwe 16:11-15. Kambilanani mmene lembali lingatithandizile mu ulaliki.

      Mph. 20: “Kugwilitsila Nchito Kabuku ka Uthenga Wabwino Pophunzitsa.” Mafunso ndi mayankho. Pambuyo pokambilana ndime 3, citani citsanzo cokonzedwa bwino coonetsa wofalitsa akugaŵila kabuku ka Uthenga Wabwino ndipo akukambilana ndime imodzi.

      Nyimbo 114 ndi Pemphelo

  • Kugwilitsila Nchito Kabuku ka Uthenga Wabwino Pophunzitsa
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015 | September
    • 1. Kodi kabuku ka Uthenga Wabwino kanalembedwa bwanji?

      1 Monga mmene tinaphunzilila mu Utumiki wathu wa Ufumu, wa July, cimodzi mwa zida zofunika pophunzitsa ndi kabuku ka Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu. Malemba ena sanagwidwe mau n’colinga cakuti eninyumba azipindula ndi phunzilo mwa kuŵelenga malemba m’Baibulo lenilenilo. Ngakhale kuti zofalitsa zathu zimalembedwa m’njila yakuti munthu angamvetsetse coonadi popanda wom’thandiza, kabukuka kanalembedwa m’njila yakuti munthu aziphunzitsidwa ndi wina wake. Conco, tikagaŵila kabukuka, tiyenela kuonetsa mwininyumba mmene timacitila phunzilo la Baibulo kuti aone mmene kuphunzila uthenga wabwino wocokela m’Baibulo kumasangalatsila.—Mat. 13:44.

Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
Tulukani
Loŵani
  • Cinyanja
  • Gawilani
  • Makonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenela Kutsatila
  • Mfundo Yosunga Cisinsi
  • Kusunga Cinsinsi
  • JW.ORG
  • Loŵani
Gawilani