CIGAWO 4 Yopulinta Nkhani Yake: Dziŵani zoyenela kucita kuti Mulungu azikukondanibe MAPHUNZILO 48 Sankhani Anzanu Mwanzelu 49 Kodi Muyenela Kucita Ciyani Kuti Banja Lanu Likhale Lacimwemwe?—Mbali 1 50 Kodi Muyenela Kucita Ciyani Kuti Banja Lanu Likhale Lacimwemwe?—Mbali 2 51 Kodi Mungamukondweletse Bwanji Yehova na Malankhulidwe Anu? 52 Cifukwa Cake Tiyenela Kusamala na Mavalidwe Komanso Maonekedwe Athu 53 Sankhani Zosangalatsa Zovomelezeka kwa Yehova 54 Udindo wa “Kapolo Wokhulupilika ndi Wanzelu” 55 Thandizani Mpingo Wanu 56 Sungani Mgwilizano wa Mpingo 57 Kodi Muyenela Kutani Mukacita Chimo Lalikulu? 58 Khalanibe Wokhulupilika kwa Yehova 59 Mukhoza Kupilila Pamene Mukuzunzidwa 60 Pitanibe Patsogolo Kuuzimu