LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 42
  • Pemphelo la Mtumiki wa Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pemphelo la Mtumiki wa Mulungu
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tikuyamikani Yehova
    Imbirani Yehova
  • Tikuyamikani Yehova
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 42

NYIMBO 42

Pemphelo la Mtumiki wa Mulungu

Yopulinta

(Aefeso 6:18)

  1. 1. Atate wathu wamphamvu yonse,

    Dzina lanu M’lungu liyeletsedwe.

    Zonse zimene mumafuna,

    Mumazipangitsa kucitika.

    Zimene mumafuna

    Sizimalepheleka.

  2. 2. Tiyamikila thandizo lanu,

    Potipatsa zimene timasowa.

    Mumatipatsa malangizo

    Kuti ise tikhale anzelu.

    Tikuyamikilani

    Cifukwa cotikonda.

  3. 3. Tikakhala na mavuto M’lungu

    Timadalila citothonzo canu.

    Pamene tili na mavuto.

    Tipempha kuti mutilimbitse.

    Conde tithandizeni,

    Tikondweletse imwe.

(Onaninso Sal. 143:10; Yoh. 21:15-17; Yak. 1:5.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani