Mlozela Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Mlonda a 2014
Tasonyeza deti la magazini imene muli nkhani
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Kulikonse kumene ndinali kupita, ndinali kukhala ndi mfuti yanga (A. Lugarà), 7/1
MAFUNSO OCOKELA KWA AŴELENGI
Kodi akulu ndi atumiki othandiza amaikidwa bwanji pa udindo? 11/15
Kodi oukitsidwa padziko lapansi “sadzakwatila kapena kukwatiwa”? (Luka 20:34-36), 8/15
Kodi Yehova sadzalola Mkristu kusoŵa cakudya? (Sal. 37:25; Mat. 6:33), 9/15
MBILI YANGA
MBONI ZA YEHOVA
NKHANI ZOPHUNZILA
Kodi Kuukitsidwa kwa Yesu Kumatanthauza Ciani kwa Ife? 11/15
Kodi Mumakhulupilila Kuti Muli ndi Coonadi? N’cifukwa Ciani? 9/15
Kodi Ulamulilo wa Yesu wa Zaka 100 Wakupindulitsani Bwanji? 1/1
Tikhale Ogwilizana Pamene Mapeto a Dzikoli Ayandikila, 12/15
Tumikilani Mulungu Mokhulupilika Panthawi ya “Masautso Ambili,” 9/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kodi Anthu Adzaononga Dziko Lapansi Kothelatu?—November-December
Kodi Cilamulo ca Mulungu kwa Aisiraeli Cinali Colungama ndi Cosakondela?—November-December
Kodi oyenda panyanja akalekale anali kupanga bwanji ngalawa zao kuti madzi asaziloŵa?—July-August
Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulila?—November-December 11/1
N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela Kuti Ufumu Ubwele?—November-December
N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela? Tizipemphela Bwanji?—July-August
N’cifukwa Ciani Zigaŵenga Anali Kuzithyola Miyendo Pozipha? 5/1
N’cifukwa Ciani Zoipa Zimacitikila Anthu Abwino?—July-August
Nkhondo Imene Inasintha Zinthu Padziko (Nkhondo yoyamba ya padziko lonse), 2/1