LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w24 August tsa. 32
  • Cidziŵitso Kwa Oŵelenga

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Cidziŵitso Kwa Oŵelenga
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
w24 August tsa. 32

Cidziŵitso Kwa Oŵelenga

Kwa Oŵelenga

M’magazini ino ya Nsanja ya Mlonda, muli nkhani zokwanila 5 zimene n’zogwilizana:

  • M’nkhani yoyamba, tidzakambilana mmene Yehova amakondela anthu, komanso zimene wacita kuti atithandize kulimbana nawo ucimo na kum’kondweletsa.

  • M’nkhani yaciŵili, tidzaphunzila zimene munthu ayenela kucita kuti alape, komanso mmene Yehova wathandizila anthu kuti alape.

  • Nkhani yacitatu idzafotokoza zimene mpingo wa ku Korinto unalangizidwa kucita na munthu amene anacita chimo lalikulu koma wosalapa.

  • M’nkhani yacinayi, tidzaphunzila mmene akulu amathandizila amene anacita chimo lalikulu.

  • M’nkhani yothela tidzaphunzila zimene mpingo ungacite kuti upitilize kucita naye mwacikondi komanso cifundo munthu amene wacotsedwa mumpingo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani