-
Levitiko 8:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni ndipo anawaveka mikanjo, anawamanga malamba apamimba komanso anawakulunga mipango kumutu,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
-