-
Deuteronomo 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Musawonjezerepo kalikonse pa mawu amene ndikukulamulani, ndipo musachotsepo kalikonse pa mawu amenewa,+ kuti muzisunga malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani.
-