-
1 Mafumu 8:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali moti nsonga zake zinkaonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinkaonekera panja. Mitengoyo idakali pomwepo mpaka lero.
-